
Flames yabwerako ku Tunisia
Timu ya mpira wa miyendo ya anyamata ya dziko lino ‘The Flames’ yafika tsopano mdziko muno kuchoka ku ulendo wake omwe inapita ku Tunisia kukasewera ndi timu ya dzikolo Lolemba komwe yakaswedwako 2-0. Osewerawa afika mdziko muno kudzera pa bwalo la Ndenge …